Malawi

Jingo Blaxie – Mila(Prod.Ron Viun & Snaz Beats)

Download | Play Now

Amati Zambiri ‎‎ is a brand built on rhythm and connection, trusted by over 13.8 million people globally.

Stream the latest hits right here, or download them to your offline storage to keep the music going wherever you are.



[LYRICS]

VERSE 1

Akati abhebhetse Uyu

Pena Abhowetse

Akati avutitse Uyu.

Ati mpaka ndipepese

Pena ndiwabhobho pena ngati wamizimu

Munthu modzi kukhala ngati ndi chi team

Amandiopsa sachedwa kupsa mtima

Pena ndimangoti bola kupeza wina

PREE HOOK

Akangoyamba Nkhani Yeah sanva pepani Yeah

(Namuzolowera ndi wa milandu)

Uyu muli makani. Simatha wamba nkhani

(Namuzolowera ndi wa milandu)

HOOK

Sungamufune akayamba zolalata

Massage Yokhayo nchikalata

Amavuta uyu Ali ndi mwano

Amabhowa akayamba Cano uyu

Eya ndi wa mila. Ndi wa milandu uyu

Olo kupepela sanva kathu

Inde muli MILA. Muli milandu uyu

Amandiopsa atha kuzapha munthu

VERSE 2

Kutiona limodzi ambiri amasilira

Ati bro muli bho mukufila

Fake smile. Koma nkati ndikulira

Mtendele palibe Akangoyamba mila

Akangoyimba phone ndimadziwa kwaola

Kungo misser call imeneyo ndi mbola

Akati Abhowetse nsaname Amabhowa

But still aka choka ndimamusowa

PREE HOOK

Akangoyamba Nkhani Yeah sanva pepani Yeah

(Namuzolowera ndi wa milandu)

Uyu muli makani. Simatha wamba nkhani

(Namuzolowera ndi wa milandu)

HOOK

Sungamufune akayamba zolalata

Massage Yokhayo nchikalata

Amavuta uyu Ali ndi mwano

Amabhowa akayamba Cano uyu

Eya ndi wa mila. Ndi wa milandu uyu

Olo kupepela sanva kathu

Inde muli MILA . Muli milandu uyu

Amandiopsa atha kuzapha munthu

BRIJ

Tatopesana aah

Tikungokangana aah (Tungokangana aaah)

Eti ngat Ana aaaah chachuluka chibwana

 (chachuluka Chibwana)

I know that you care ukamalalata

Zimangobhowa poti sundipatsa mpata

Chikondi cha ifeyo chi a sowa bata

But still ndimakukonda iwe ndi wanga.

HOOK

Sungamufune akayamba zolalata

Massage Yokhayo nchikalata

Amavuta uyu Ali ndi mwano

Amabhowa akayamba Cano uyu

Eya ndi wa mila. Ndi wa milandu uyu

Olo kupepela sanva kathu

Inde muli MILA . Muli milandu uyu

Amandiopsa atha kuzapha munthu

Sungamufune akayamba zolalata

Massage Yokhayo nchikalata

Amavuta uyu Ali ndi mwano

Amabhowa akayamba Cano uyu

Eya ndi wa mila. Ndi wa milandu uyu

Olo kupepela sanva kathu

Inde muli MILA . Muli milandu uyu

Amandiopsa atha kuzapha munthu

 

Stream and download below!

WhatsApp Channel Follow Now

Download Abudu Kadango – Ndakana ft Fred Mw

Download Abudu Kadango – Anene Okha

Disclaimer

Welcome to amatizambiri.com. This website is primarily dedicated to music sharing, but may also feature other content related to entertainment and media. By using this website, you agree to comply with the following terms and conditions:

 

1. Intellectual Property

All content on this website, including music files, images, text, and other media, is protected by copyright and intellectual property laws. You are not allowed to:

– Repost, re-upload, or redistribute any content from this website in any form.

– Use downloaded files for commercial purposes without explicit permission.

– Claim ownership of any content posted on this website.

Violation of these rules may result in legal action.

 

2. Use of Downloaded Files

Files downloaded from this website are intended for personal, non-commercial use only. By downloading content, you agree that you will not share, sell, or distribute these files in any way.

 

3. Reporting Unauthorized Content

If your content has been posted or uploaded to amatizambiri.com without your consent, you have the right to request its removal.

To report unauthorized content:

– Click [Here] to contact us.

– Provide details of the content and proof of ownership.

We will review your request and remove the content within 3 days of receiving your notice.

 

4. Limitation of Liability

While we strive to provide accurate and reliable content, amatizambiri.com is not responsible for any errors, omissions, or damages arising from the use of this website.

By using this site, you agree that your use is at your own risk.

 

5. Third-Party Links

This website may contain links to third-party websites for convenience or reference. We do not endorse or take responsibility for any content, services, or products available on these external sites.

 

6. Updates to Disclaimer

We reserve the right to update or modify this disclaimer at any time. Changes will be effective immediately upon posting on this page. We encourage users to review this page regularly.

Thank you for visiting AmatiZambiri.com. By using this website, you agree to the terms outlined in this disclaimer.

Armsochi

I'm Armsochi, a Lilongwe-based talent promoter. I help musicians and poets quickly reach a wider audience online, boosting downloads. Contact: +265 884 790 698 / +265 992 349 991.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Related Songs

Back to top button